Talk:Samuel Kawale
Appearance
This article is rated Start-class on Wikipedia's content assessment scale. It is of interest to the following WikiProjects: | ||||||||||||||||||||||||
|
Honorable
[edit]Zipangizo za ulimi zotsika mtengo. Boma linatiganizila ife a Malawi osaukitsitsa kuti tithe kufikila kugula zipangozozi kuno kwathu kwa Chimpumbulu T/A Chitukula, Lilongwe koma zomwe zikuchitika ndi dzinyengo anthu omwe mwawatuma kuti adzatigulitse zipangizozi kuti munthu agule ayeneleka kupelekanso ndalama ya lunch kuwonjezela apo omwe akugula zipangizozi ndi mavenda okha okha ife anthu akumudzi tikupempha kuti mutibweletsele achitetezo.Mwina anthu omwe mwawatuma wa ndi a opposition iyi a kupangayi ndi dikampeni yoti a Malawi ade kukhosi ndi Boma lomwe likulamulilali.Chonde bwana tithandizeni 137.196.0.28 (talk) 03:18, 13 November 2024 (UTC)